Miyambo 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndili ndi malangizo+ ndi nzeru zopindulitsa.+ Ndimamvetsa zinthu,+ ndiponso ndili ndi mphamvu.+ Miyambo 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Wanzeru amakwera mzinda wa anthu amphamvu, kuti athetse mphamvu imene mzindawo umadalira.+ Mlaliki 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nzeru zimapangitsa munthu kukhala wamphamvu kuposa atsogoleri 10 amphamvu amene ali mumzinda.+
14 Ine ndili ndi malangizo+ ndi nzeru zopindulitsa.+ Ndimamvetsa zinthu,+ ndiponso ndili ndi mphamvu.+