Mlaliki 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nzeru zimapangitsa munthu kukhala wamphamvu kuposa atsogoleri 10 amphamvu amene ali mumzinda.+ Mlaliki 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ineyo ndinati: “Nzeru n’zabwino kuposa mphamvu,+ koma nzeru za munthu wosauka zimanyozedwa ndipo anthu samvera mawu ake.”+ 2 Akorinto 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti zida za nkhondo yathu si zochokera m’dziko lino,+ koma ndi zida zamphamvu zimene Mulungu watipatsa,+ zimene zimatha kugwetsa zinthu zozikika molimba.
16 Choncho ineyo ndinati: “Nzeru n’zabwino kuposa mphamvu,+ koma nzeru za munthu wosauka zimanyozedwa ndipo anthu samvera mawu ake.”+
4 Pakuti zida za nkhondo yathu si zochokera m’dziko lino,+ koma ndi zida zamphamvu zimene Mulungu watipatsa,+ zimene zimatha kugwetsa zinthu zozikika molimba.