Miyambo 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Wanzeru amakwera mzinda wa anthu amphamvu, kuti athetse mphamvu imene mzindawo umadalira.+ Miyambo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu amene amagwiritsa ntchito mphamvu zake mwanzeru ndiye mwamuna wamphamvu,+ ndipo munthu wodziwa zinthu amachulukitsa mphamvu zake.+ Mlaliki 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nzeru zimapangitsa munthu kukhala wamphamvu kuposa atsogoleri 10 amphamvu amene ali mumzinda.+ Mlaliki 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndi bwino kukhala ndi nzeru kuposa kukhala ndi zida zomenyera nkhondo, ndipo wochimwa mmodzi yekha akhoza kuwononga zabwino zochuluka.+
5 Munthu amene amagwiritsa ntchito mphamvu zake mwanzeru ndiye mwamuna wamphamvu,+ ndipo munthu wodziwa zinthu amachulukitsa mphamvu zake.+
18 Ndi bwino kukhala ndi nzeru kuposa kukhala ndi zida zomenyera nkhondo, ndipo wochimwa mmodzi yekha akhoza kuwononga zabwino zochuluka.+