1 Mafumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+ Maliko 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chake ndikukuuzani kuti, Pa zinthu zonse zimene mukupempherera ndi kupempha, khalani ndi chikhulupiriro ngati kuti mwazilandira kale, ndipo mudzazilandiradi.+ 1 Yohane 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ndipo chilichonse chimene tingapemphe, iye adzatipatsa,+ chifukwa tikusunga malamulo ake ndi kuchita zinthu zomukondweretsa.+
9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+
24 N’chifukwa chake ndikukuuzani kuti, Pa zinthu zonse zimene mukupempherera ndi kupempha, khalani ndi chikhulupiriro ngati kuti mwazilandira kale, ndipo mudzazilandiradi.+
22 ndipo chilichonse chimene tingapemphe, iye adzatipatsa,+ chifukwa tikusunga malamulo ake ndi kuchita zinthu zomukondweretsa.+