2 Samueli 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ine mtumiki wanu ndinaganiza kuti, ‘Mawu a mbuyanga mfumu andipatsa mpumulo.’ Pakuti inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, wokhoza kusiyanitsa chabwino ndi choipa.+ Ndipo Yehova Mulungu wanu akhale nanu.” Aheberi 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu okhwima mwauzimu, amene pogwiritsa ntchito mphamvu zawo za kuzindikira,+ aphunzitsa mphamvuzo kusiyanitsa choyenera ndi chosayenera.+
17 ine mtumiki wanu ndinaganiza kuti, ‘Mawu a mbuyanga mfumu andipatsa mpumulo.’ Pakuti inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, wokhoza kusiyanitsa chabwino ndi choipa.+ Ndipo Yehova Mulungu wanu akhale nanu.”
14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu okhwima mwauzimu, amene pogwiritsa ntchito mphamvu zawo za kuzindikira,+ aphunzitsa mphamvuzo kusiyanitsa choyenera ndi chosayenera.+