Yesaya 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye azidzadya mafuta a mkaka ndi uchi pofika nthawi imene adzadziwe kukana choipa ndi kusankha chabwino.+ Aroma 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti anthu onse+ adziwa kuti ndinu omvera. Choncho ndikusangalala chifukwa cha inu. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru+ pa zinthu zabwino, ndi osadziwa+ kanthu pa zinthu zoipa.+ Afilipi 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chitani zimenezi kuti muzitsimikizira kuti zinthu zofunika kwambiri ndi ziti,+ kuti mukhale opanda cholakwa+ ndi osakhumudwitsa+ ena kufikira tsiku la Khristu. 1 Atesalonika 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsimikizirani zinthu zonse.+ Gwirani mwamphamvu chimene chili chabwino.+
15 Iye azidzadya mafuta a mkaka ndi uchi pofika nthawi imene adzadziwe kukana choipa ndi kusankha chabwino.+
19 Pakuti anthu onse+ adziwa kuti ndinu omvera. Choncho ndikusangalala chifukwa cha inu. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru+ pa zinthu zabwino, ndi osadziwa+ kanthu pa zinthu zoipa.+
10 Chitani zimenezi kuti muzitsimikizira kuti zinthu zofunika kwambiri ndi ziti,+ kuti mukhale opanda cholakwa+ ndi osakhumudwitsa+ ena kufikira tsiku la Khristu.