Yeremiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+ 1 Akorinto 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abale, musakhale ana aang’ono pa luntha la kuzindikira,+ koma khalani tiana pa zoipa,+ ndipo pa luntha la kuzindikira khalani aakulu msinkhu.+
22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+
20 Abale, musakhale ana aang’ono pa luntha la kuzindikira,+ koma khalani tiana pa zoipa,+ ndipo pa luntha la kuzindikira khalani aakulu msinkhu.+