1 Samueli 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma zimenezi zinamuipira Samueli, chifukwa iwo anati: “Utipatse mfumu yoti izitiweruza.” Pamenepo Samueli anayamba kupemphera kwa Yehova.+
6 Koma zimenezi zinamuipira Samueli, chifukwa iwo anati: “Utipatse mfumu yoti izitiweruza.” Pamenepo Samueli anayamba kupemphera kwa Yehova.+