Salimo 143:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiphunzitseni kuchita chifuniro chanu,+Pakuti inu ndinu Mulungu wanga.+Mzimu wanu ndi wabwino.+Unditsogolere m’dziko la olungama.+ Mateyu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ufumu+ wanu ubwere. Chifuniro chanu+ chichitike, monga kumwamba, chimodzimodzinso pansi pano.+
10 Ndiphunzitseni kuchita chifuniro chanu,+Pakuti inu ndinu Mulungu wanga.+Mzimu wanu ndi wabwino.+Unditsogolere m’dziko la olungama.+