Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pa tsikuli, Yehova anachititsa Yoswa kukhala wamkulu m’maso mwa Aisiraeli onse,+ ndipo anayamba kumuopa monga mmene anaopera Mose masiku onse a moyo wake.+

  • 1 Samueli 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Choncho Samueli anafuulira Yehova,+ moti Yehova anadzetsa mabingu ndi mvula tsiku limenelo.+ Pamenepo anthu onse anachita mantha kwambiri ndi Yehova ndiponso ndi Samueli.

  • 1 Mbiri 29:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Akalonga onse+ ndi amuna amphamvu,+ ndiponso ana onse a Mfumu Davide,+ anali kugonjera Solomo mfumu.

  • Salimo 72:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Iwo adzakuopani nthawi zonse pamene dzuwa likuwala,+

      Adzakuopani ku mibadwomibadwo pamene mwezi uli kuthambo.+

  • Miyambo 24:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mwana wanga uziopa Yehova ndiponso mfumu.+ Usamakhale pagulu la anthu ofuna kuti zinthu zisinthe,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena