Yoswa 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndiyamba kukukuza pamaso pa Aisiraeli onse,+ n’cholinga choti adziwe kuti monga mmene ndinakhalira ndi Mose,+ ndidzakhalanso ndi iwe.+ Salimo 75:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ndiye woweruza.+Amatsitsa wina ndi kukweza wina.+
7 Ndipo Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndiyamba kukukuza pamaso pa Aisiraeli onse,+ n’cholinga choti adziwe kuti monga mmene ndinakhalira ndi Mose,+ ndidzakhalanso ndi iwe.+