Yoswa 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa tsikuli, Yehova anachititsa Yoswa kukhala wamkulu m’maso mwa Aisiraeli onse,+ ndipo anayamba kumuopa monga mmene anaopera Mose masiku onse a moyo wake.+
14 Pa tsikuli, Yehova anachititsa Yoswa kukhala wamkulu m’maso mwa Aisiraeli onse,+ ndipo anayamba kumuopa monga mmene anaopera Mose masiku onse a moyo wake.+