Salimo 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo kumwamba kukunena za chilungamo chake,+Pakuti Mulungu ndiye Woweruza.+ [Seʹlah.] Salimo 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo mtundu wa anthu udzati:+ “Ndithudi wolungama adzalandira mphoto.+Ndithudi pali Mulungu amene akuweruza dziko lapansi.”+
11 Ndipo mtundu wa anthu udzati:+ “Ndithudi wolungama adzalandira mphoto.+Ndithudi pali Mulungu amene akuweruza dziko lapansi.”+