Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.] Salimo 98:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu molungama.+ Aheberi 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakuti timamudziwa amene anati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzabwezera ndine.”+ Ndiponso: “Yehova adzaweruza anthu ake.”+
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]
9 Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu molungama.+
30 Pakuti timamudziwa amene anati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzabwezera ndine.”+ Ndiponso: “Yehova adzaweruza anthu ake.”+