Deuteronomo 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye adzapitiriza kuyenda nanu.+ Sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono. Choncho musaope kapena kuchita mantha.”+ Yoswa 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+ Yoswa 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Monga tinamvera Mose m’chilichonse, tidzakhalanso omvera kwa inu. Yehova Mulungu wanu akhale nanu+ mmene anakhalira ndi Mose.+
8 Yehova ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye adzapitiriza kuyenda nanu.+ Sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono. Choncho musaope kapena kuchita mantha.”+
5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+
17 Monga tinamvera Mose m’chilichonse, tidzakhalanso omvera kwa inu. Yehova Mulungu wanu akhale nanu+ mmene anakhalira ndi Mose.+