Ekisodo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Mulungu anati: “Chifukwa ndidzakhala nawe.+ Ndipo chizindikiro chako chakuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi:+ Pambuyo powatulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira Mulungu woona paphiri lino.”+ Yoswa 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndiyamba kukukuza pamaso pa Aisiraeli onse,+ n’cholinga choti adziwe kuti monga mmene ndinakhalira ndi Mose,+ ndidzakhalanso ndi iwe.+
12 Pamenepo Mulungu anati: “Chifukwa ndidzakhala nawe.+ Ndipo chizindikiro chako chakuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi:+ Pambuyo powatulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira Mulungu woona paphiri lino.”+
7 Ndipo Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndiyamba kukukuza pamaso pa Aisiraeli onse,+ n’cholinga choti adziwe kuti monga mmene ndinakhalira ndi Mose,+ ndidzakhalanso ndi iwe.+