Ekisodo 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ananyamuka ku Refidimu+ n’kulowa m’chipululu cha Sinai+ ndi kumanga msasa wawo m’chipululumo. Aisiraeli anamanga msasawo pafupi ndi phiri la Sinai.+ Deuteronomo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Choncho anthu inu munayandikira ndi kuimirira m’munsi mwa phiri. Phiri limenelo linali kuyaka moto mpaka kumwamba, ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+
2 Ananyamuka ku Refidimu+ n’kulowa m’chipululu cha Sinai+ ndi kumanga msasa wawo m’chipululumo. Aisiraeli anamanga msasawo pafupi ndi phiri la Sinai.+
11 “Choncho anthu inu munayandikira ndi kuimirira m’munsi mwa phiri. Phiri limenelo linali kuyaka moto mpaka kumwamba, ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+