Ekisodo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo khamu lonse la ana a Isiraeli linanyamuka kuchipululu cha Sini.+ Ulendowo anaugawa mitundamitunda, malinga ndi mmene Yehova anawauzira,+ ndipo anamanga msasa wawo pa Refidimu.+ Koma pamenepo panalibe madzi akumwa.
17 Ndipo khamu lonse la ana a Isiraeli linanyamuka kuchipululu cha Sini.+ Ulendowo anaugawa mitundamitunda, malinga ndi mmene Yehova anawauzira,+ ndipo anamanga msasa wawo pa Refidimu.+ Koma pamenepo panalibe madzi akumwa.