1 Mafumu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Patapita masiku ambiri,+ mawu a Yehova anafikira Eliya m’chaka chachitatu, kuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula padziko lapansi.”+
18 Patapita masiku ambiri,+ mawu a Yehova anafikira Eliya m’chaka chachitatu, kuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula padziko lapansi.”+