Luka 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwachitsanzo, ndikukuuzani ndithu kuti, Munali akazi ambiri amasiye mu Isiraeli m’masiku a Eliya, pamene kumwamba kunatsekedwa zaka zitatu ndi miyezi 6, mwakuti m’dziko lonse munagwa njala yaikulu.+ Yakobo 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Eliya anali munthu monga ife tomwe,+ komabe anapemphera kuti mvula isagwe,+ ndipo mvula sinagwe kumeneko kwa zaka zitatu ndi miyezi 6.
25 Mwachitsanzo, ndikukuuzani ndithu kuti, Munali akazi ambiri amasiye mu Isiraeli m’masiku a Eliya, pamene kumwamba kunatsekedwa zaka zitatu ndi miyezi 6, mwakuti m’dziko lonse munagwa njala yaikulu.+
17 Eliya anali munthu monga ife tomwe,+ komabe anapemphera kuti mvula isagwe,+ ndipo mvula sinagwe kumeneko kwa zaka zitatu ndi miyezi 6.