1 Mafumu 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Nyamuka, upite ku Zarefati+ m’dziko la Sidoni ukakhale kumeneko. Ine ndikalamula mayi wina wa kumeneko, mkazi wamasiye, kuti azikakupatsa chakudya.” 1 Mafumu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Patapita masiku ambiri,+ mawu a Yehova anafikira Eliya m’chaka chachitatu, kuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula padziko lapansi.”+ Yakobo 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Eliya anali munthu monga ife tomwe,+ komabe anapemphera kuti mvula isagwe,+ ndipo mvula sinagwe kumeneko kwa zaka zitatu ndi miyezi 6.
9 “Nyamuka, upite ku Zarefati+ m’dziko la Sidoni ukakhale kumeneko. Ine ndikalamula mayi wina wa kumeneko, mkazi wamasiye, kuti azikakupatsa chakudya.”
18 Patapita masiku ambiri,+ mawu a Yehova anafikira Eliya m’chaka chachitatu, kuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula padziko lapansi.”+
17 Eliya anali munthu monga ife tomwe,+ komabe anapemphera kuti mvula isagwe,+ ndipo mvula sinagwe kumeneko kwa zaka zitatu ndi miyezi 6.