2 Samueli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 munthu wina atandibweretsera uthenga wakuti, ‘Sauli wafa,’+ poganiza kuti wabweretsa uthenga wabwino, ine ndinamugwira nʼkumupha+ ku Zikilaga. Malipiro a uthenga umene anabweretsa anali amenewo.
10 munthu wina atandibweretsera uthenga wakuti, ‘Sauli wafa,’+ poganiza kuti wabweretsa uthenga wabwino, ine ndinamugwira nʼkumupha+ ku Zikilaga. Malipiro a uthenga umene anabweretsa anali amenewo.