Salimo 94:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye adzawabwezera zoipa zawo,+Ndipo adzawakhalitsa chete mwa kuwadzetsera masoka okonza okha.+Yehova Mulungu wathu adzawakhalitsa chete.+ Yesaya 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti anthu sapuntha chitowe chakuda ndi chida chopunthira+ ndipo pachitowe chamtundu wina sayendetsapo mawilo a ngolo yopunthira mbewu. Nthawi zambiri chitowe chakuda amachipuntha ndi ndodo+ ndipo chitowe chamtundu wina amachipuntha ndi kamtengo.
23 Iye adzawabwezera zoipa zawo,+Ndipo adzawakhalitsa chete mwa kuwadzetsera masoka okonza okha.+Yehova Mulungu wathu adzawakhalitsa chete.+
27 Pakuti anthu sapuntha chitowe chakuda ndi chida chopunthira+ ndipo pachitowe chamtundu wina sayendetsapo mawilo a ngolo yopunthira mbewu. Nthawi zambiri chitowe chakuda amachipuntha ndi ndodo+ ndipo chitowe chamtundu wina amachipuntha ndi kamtengo.