Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha. Salimo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mavuto ake adzabwerera pamutu pake,+Ndipo chiwawa chake chidzatsikira paliwombo pake.+ Miyambo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma oipa adzachotsedwa padziko lapansi+ ndipo achinyengo adzazulidwamo.+ Miyambo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Woipa adzagwidwa ndi zolakwa zake zomwe,+ ndipo adzamangidwa m’zingwe za tchimo lake lomwe.+ 2 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chiweruzo cha Mulunguchi n’cholungama chifukwa akubwezera masautso kwa amene amakusautsani.+