Yesaya 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa chitowe chakuda sachipuntha ndi chida chopunthira,+Ndipo pachitowe chamtundu wina sayendetsapo mawilo a ngolo yopunthira mbewu. Mʼmalomwake, chitowe chakuda amachipuntha ndi ndodo,Ndipo chitowe chamtundu wina amachipuntha ndi kamtengo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:27 Yesaya 1, ptsa. 296, 301 Galamukani!,2/8/1991, tsa. 30
27 Chifukwa chitowe chakuda sachipuntha ndi chida chopunthira,+Ndipo pachitowe chamtundu wina sayendetsapo mawilo a ngolo yopunthira mbewu. Mʼmalomwake, chitowe chakuda amachipuntha ndi ndodo,Ndipo chitowe chamtundu wina amachipuntha ndi kamtengo.