Yesaya 41:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+ chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano. Udzapondaponda mapiri n’kuwaphwanya, ndipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.+ Amosi 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Damasiko+ anapanduka mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anapuntha Giliyadi+ ndi zida zachitsulo zopunthira.
15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+ chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano. Udzapondaponda mapiri n’kuwaphwanya, ndipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.+
3 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Damasiko+ anapanduka mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anapuntha Giliyadi+ ndi zida zachitsulo zopunthira.