Yesaya 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+ Yesaya 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 popeza mwanayo asanadziwe kuitana+ kuti, ‘Ababa!’ kapena ‘Amama!’ anthu adzanyamula chuma cha ku Damasiko ndi katundu wolandidwa ku Samariya n’kupita naye pamaso pa mfumu ya Asuri.”+
8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+
4 popeza mwanayo asanadziwe kuitana+ kuti, ‘Ababa!’ kapena ‘Amama!’ anthu adzanyamula chuma cha ku Damasiko ndi katundu wolandidwa ku Samariya n’kupita naye pamaso pa mfumu ya Asuri.”+