2 Mafumu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’chaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ n’kutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala+ ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani,+ ndiponso m’mizinda ya Amedi.+ Hoseya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Gomeri anatenganso pakati ndi kubereka mwana wamkazi. Ndiyeno Mulungu anauza Hoseya kuti: “Mwanayu umupatse dzina lakuti Lo-ruhama,*+ pakuti sindidzachitiranso chifundo+ anthu a m’nyumba ya Isiraeli, chifukwa ndidzawathamangitsa.+
6 M’chaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ n’kutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala+ ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani,+ ndiponso m’mizinda ya Amedi.+
6 Kenako Gomeri anatenganso pakati ndi kubereka mwana wamkazi. Ndiyeno Mulungu anauza Hoseya kuti: “Mwanayu umupatse dzina lakuti Lo-ruhama,*+ pakuti sindidzachitiranso chifundo+ anthu a m’nyumba ya Isiraeli, chifukwa ndidzawathamangitsa.+