2 Mafumu 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pambuyo pake mfumu ya Asuri+ inatenga Aisiraeli n’kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala,+ ndi ku Habori+ pafupi ndi mtsinje wa Gozani, ndiponso m’mizinda ya Amedi.+
11 Pambuyo pake mfumu ya Asuri+ inatenga Aisiraeli n’kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala,+ ndi ku Habori+ pafupi ndi mtsinje wa Gozani, ndiponso m’mizinda ya Amedi.+