Amosi 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+ ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamabedi lidzatha. Amosi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+
7 “Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+ ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamabedi lidzatha.
4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+