Deuteronomo 28:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Udzabereka ana aamuna ndi ana aakazi, koma sadzapitiriza kukhala ako chifukwa adzatengedwa kupita ku ukapolo.+ Amosi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+
41 Udzabereka ana aamuna ndi ana aakazi, koma sadzapitiriza kukhala ako chifukwa adzatengedwa kupita ku ukapolo.+
5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+