Yesaya 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tinthambi take tikadzauma, akazi obwera kumeneko adzatithyola n’kutiyatsa.+ Pakuti anthuwo si omvetsa zinthu.+ N’chifukwa chake yemwe anawapanga sadzawachitira chifundo, ndipo yemwe anawaumba sadzawakomera mtima.+ 1 Petulo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti kale simunali mtundu, koma tsopano ndinu mtundu wa anthu a Mulungu.+ Munali anthu amene sanakuchitireni chifundo, koma tsopano ndinu amene mwachitiridwa chifundo.+
11 Tinthambi take tikadzauma, akazi obwera kumeneko adzatithyola n’kutiyatsa.+ Pakuti anthuwo si omvetsa zinthu.+ N’chifukwa chake yemwe anawapanga sadzawachitira chifundo, ndipo yemwe anawaumba sadzawakomera mtima.+
10 Pakuti kale simunali mtundu, koma tsopano ndinu mtundu wa anthu a Mulungu.+ Munali anthu amene sanakuchitireni chifundo, koma tsopano ndinu amene mwachitiridwa chifundo.+