Deuteronomo 32:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti iwo ndi mtundu wopanda nzeru,+Ndipo ndi osazindikira.+ Yesaya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ng’ombe yamphongo imam’dziwa bwino munthu amene anaigula, ndipo bulu amadziwa chinthu chimene mbuye wake amam’dyetseramo. Koma Isiraeli sandidziwa,+ ndipo anthu anga sanachite zinthu mozindikira.”+ Yeremiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+ Hoseya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+
3 Ng’ombe yamphongo imam’dziwa bwino munthu amene anaigula, ndipo bulu amadziwa chinthu chimene mbuye wake amam’dyetseramo. Koma Isiraeli sandidziwa,+ ndipo anthu anga sanachite zinthu mozindikira.”+
22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+
6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+