Salimo 106:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mofulumira anaiwala ntchito zake,+Iwo sanayembekezere malangizo ake.+ Salimo 107:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa anachita zinthu mopandukira+ mawu a Mulungu,+Ndipo ananyoza malangizo a Wam’mwambamwamba.+ Luka 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)
11 Chifukwa anachita zinthu mopandukira+ mawu a Mulungu,+Ndipo ananyoza malangizo a Wam’mwambamwamba.+
30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)