2 Mbiri 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova anapitiriza kulankhula kwa Manase ndi anthu ake, koma iwo sanamvere.+ Salimo 73:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mudzanditsogolera ndi malangizo anu,+Ndipo pambuyo pake mudzanditenga ndi kundipatsa ulemerero.+ Miyambo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 mukungonyalanyaza malangizo anga onse,+ ndipo simunamvere kudzudzula kwanga,+ Luka 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)
30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)