Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 80:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Watenthedwa ndi moto ndi kudulidwa.+

      Iwo amawonongeka ndi kudzudzula kwa pankhope panu.+

  • Yesaya 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 M’dzikolo mudzakhalabe chakhumi+ ndipo chidzakhalanso chinthu chofunika kuchitentha ngati mtengo waukulu, ndiponso ngati chimtengo chachikulu, chimene chikadulidwa+ pamatsala chitsa.+ Mbewu yopatulika idzakhala chitsa chake.”+

  • Ezekieli 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Mofanana ndi mtengo wa mpesa umene uli pakati pa nkhalango, umene ndaupereka kuti uzikhala nkhuni pamoto, ndaperekanso anthu okhala mu Yerusalemu.+

  • Mateyu 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nkhwangwa+ yaikidwa kale pamizu yamitengo. Chotero mtengo uliwonse wosabala zipatso zabwino udulidwa+ ndi kuponyedwa pamoto.+

  • Yohane 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena