Ezekieli 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Mofanana ndi mtengo wa mpesa womwe uli pakati pa mitengo yamʼnkhalango, umene ndaupereka kuti ukhale nkhuni, ndidzachitanso chimodzimodzi ndi anthu amene akukhala mu Yerusalemu.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:6 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
6 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Mofanana ndi mtengo wa mpesa womwe uli pakati pa mitengo yamʼnkhalango, umene ndaupereka kuti ukhale nkhuni, ndidzachitanso chimodzimodzi ndi anthu amene akukhala mu Yerusalemu.+