Ezekieli 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Mofanana ndi mtengo wa mpesa umene uli pakati pa nkhalango, umene ndaupereka kuti uzikhala nkhuni pamoto, ndaperekanso anthu okhala mu Yerusalemu.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:6 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
6 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Mofanana ndi mtengo wa mpesa umene uli pakati pa nkhalango, umene ndaupereka kuti uzikhala nkhuni pamoto, ndaperekanso anthu okhala mu Yerusalemu.+