Salimo 79:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Haa! Inu Yehova, mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+Kodi mkwiyo wanu udzakhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+ Yeremiya 52:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu ndi nyumba zonse za mu Yerusalemu.+ Anatenthanso nyumba iliyonse ya munthu wotchuka.+
5 Haa! Inu Yehova, mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+Kodi mkwiyo wanu udzakhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+
13 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu ndi nyumba zonse za mu Yerusalemu.+ Anatenthanso nyumba iliyonse ya munthu wotchuka.+