Yesaya 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tinthambi take tikadzauma,Akazi adzabwera kudzatithyolaNʼkukakolezera moto. Anthu awa samvetsa zinthu,+ Nʼchifukwa chake amene anawapanga sadzawachitira chifundo,Ndipo amene anawaumba sadzawakomera mtima.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:11 Yesaya 1, tsa. 285
11 Tinthambi take tikadzauma,Akazi adzabwera kudzatithyolaNʼkukakolezera moto. Anthu awa samvetsa zinthu,+ Nʼchifukwa chake amene anawapanga sadzawachitira chifundo,Ndipo amene anawaumba sadzawakomera mtima.+