Numeri 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mizindayo ikakhale kothawirako munthu wopha mnzake amene akuthawa wobwezera magazi,+ kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe kufikira ataima pamaso pa oweruza kuti aweruzidwe.+ Numeri 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Wobwezera magazi+ ndi amene ayenera kupha wakupha munthuyo. Akadzangom’peza, wobwezera magaziyo adzamuphe.
12 Mizindayo ikakhale kothawirako munthu wopha mnzake amene akuthawa wobwezera magazi,+ kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe kufikira ataima pamaso pa oweruza kuti aweruzidwe.+
19 “‘Wobwezera magazi+ ndi amene ayenera kupha wakupha munthuyo. Akadzangom’peza, wobwezera magaziyo adzamuphe.