Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Koma pakakhala munthu wodana+ ndi mnzake amene wabisalira ndi kuukira mnzakeyo panjira n’kumukantha ndipo wafa,+ iye n’kuthawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi,

  • Deuteronomo 19:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 akulu a mumzinda wakwawo azitumiza anthu kukam’tenga kumeneko, ndipo azim’pereka m’manja mwa wobwezera magazi kuti afe ndithu.+

  • Yoswa 20:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ngati wobwezera magazi atam’thamangitsa, akuluwo asapereke wopha munthuyo m’manja mwa wobwezera magaziyo,+ chifukwa iye sanaphe munthu mnzakeyo mwadala, ndiponso sankadana naye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena