Yoswa 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngati wobwezera magazi amene akumuthamangitsa wafika, akuluwo asamapereke wopha munthuyo kwa wobwezera magaziyo, chifukwa iye sanaphe munthuyo mwadala ndipo sankadana naye.+
5 Ngati wobwezera magazi amene akumuthamangitsa wafika, akuluwo asamapereke wopha munthuyo kwa wobwezera magaziyo, chifukwa iye sanaphe munthuyo mwadala ndipo sankadana naye.+