Yoswa 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngati wobwezera magazi atam’thamangitsa, akuluwo asapereke wopha munthuyo m’manja mwa wobwezera magaziyo,+ chifukwa iye sanaphe munthu mnzakeyo mwadala, ndiponso sankadana naye.+
5 Ngati wobwezera magazi atam’thamangitsa, akuluwo asapereke wopha munthuyo m’manja mwa wobwezera magaziyo,+ chifukwa iye sanaphe munthu mnzakeyo mwadala, ndiponso sankadana naye.+