Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Yakobo anatsogoza amithenga+ ake powatumiza kwa Esau m’bale wake, kudziko la Seiri,+ kudera la Edomu.+

  • Genesis 36:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Esau analinso kutchedwa Edomu.+

  • Deuteronomo 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Pamene Wam’mwambamwamba anapereka cholowa kwa mitundu,+

      Pamene analekanitsa ana a Adamu,+

      Anaika malire a anthu+

      Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+

  • Yoswa 24:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Isaki anabereka Yakobo ndi Esau.+ Pambuyo pake Esau ndinam’patsa phiri la Seiri kuti likhale lake.+ Kenako, Yakobo ndi ana ake anapita ku Iguputo.+

  • 2 Mbiri 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano taonani zimene akuchita ana a Amoni,+ ana a Mowabu+ ndi a kudera lamapiri la Seiri.+ Inu simunalole kuti Aisiraeli alowe m’dziko lawo pamene anali kutuluka m’dziko la Iguputo ndipo anawasiya osawawononga.+

  • Machitidwe 17:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mtundu wonse wa anthu,+ kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anakhazikitsa nthawi zoikidwiratu+ komanso anaika malire achikhalire a malo oti anthu azikhala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena