Genesis 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndipatseko chakudya chofiiracho pang’ono, icho chofiiracho! Ndatopatu ine!” Ndiye chifukwa chake anatchedwa Edomu.*+ Oweruza 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova, pamene munayenda kuchokera ku Seiri,+Pamene munaguba kuchokera kudera la Edomu,+Dziko linagwedezeka,+ kumwamba kunagwetsa madzi,+Mitambo inagwetsa madzi.
30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndipatseko chakudya chofiiracho pang’ono, icho chofiiracho! Ndatopatu ine!” Ndiye chifukwa chake anatchedwa Edomu.*+
4 Yehova, pamene munayenda kuchokera ku Seiri,+Pamene munaguba kuchokera kudera la Edomu,+Dziko linagwedezeka,+ kumwamba kunagwetsa madzi,+Mitambo inagwetsa madzi.