Genesis 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anapitiriza kuti: “Ine ndine Mulungu woona,+ Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakukuza kukhala mtundu waukulu.+ Salimo 105:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Isiraeli anapita ku Iguputo,+Yakobo anakhala monga mlendo m’dziko la Hamu.+ Machitidwe 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yakobo anapita ku Iguputo+ kumene iye ndi makolo athu+ aja anamwalirira.+
3 Mulungu anapitiriza kuti: “Ine ndine Mulungu woona,+ Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakukuza kukhala mtundu waukulu.+