Genesis 49:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yakobo atamaliza kulangiza ana akewo, anabwezeranso miyendo yake pabedi, n’kumwalira. Kenako anaikidwa m’manda n’kugona limodzi ndi makolo ake.+
33 Yakobo atamaliza kulangiza ana akewo, anabwezeranso miyendo yake pabedi, n’kumwalira. Kenako anaikidwa m’manda n’kugona limodzi ndi makolo ake.+