Genesis 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako, Abulahamu anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino, wautali ndi wokhutira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake.+ Salimo 116:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’maso mwa YehovaImfa ya anthu ake okhulupirika ndi nkhani yaikulu.+ Mateyu 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo’?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+ Machitidwe 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yakobo anapita ku Iguputo+ kumene iye ndi makolo athu+ aja anamwalirira.+
8 Kenako, Abulahamu anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino, wautali ndi wokhutira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake.+
32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo’?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+