Genesis 35:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Isaki anamwalira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake. Anamwalira ali wokalamba, wokhutira ndi masiku ake.+ Ana ake, Esau ndi Yakobo, anamuika m’manda.+ Miyambo 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti ine ndidzachititsa kuti masiku ako akhale ambiri+ ndipo zaka za moyo wako zidzawonjezeredwa.+
29 Kenako Isaki anamwalira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake. Anamwalira ali wokalamba, wokhutira ndi masiku ake.+ Ana ake, Esau ndi Yakobo, anamuika m’manda.+
11 Pakuti ine ndidzachititsa kuti masiku ako akhale ambiri+ ndipo zaka za moyo wako zidzawonjezeredwa.+